Yesaya 49:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 koma ana ako amene unabereka ana ena onse atamwalira,+ adzakuuza kuti, ‘Malowa atichepera.+ Tipezereni malo oti tikhalemo.’+ Yesaya 54:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kulitsa hema wako.+ Nsalu za hema wako wamkulu zitambasulidwe. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za hema wako ndipo ulimbitse zikhomo zake.+
20 koma ana ako amene unabereka ana ena onse atamwalira,+ adzakuuza kuti, ‘Malowa atichepera.+ Tipezereni malo oti tikhalemo.’+
2 “Kulitsa hema wako.+ Nsalu za hema wako wamkulu zitambasulidwe. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za hema wako ndipo ulimbitse zikhomo zake.+