Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”

  • 2 Mafumu 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano ana+ a aneneri anauza Elisa kuti: “Taonani, malo+ amene tikukhala pamaso panu pano tikupanikizanapo.+

  • Yesaya 54:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 “Iwe mkazi wosabereka amene sunaberekepo mwana,+ fuula mokondwa!+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ kondwera! Fuula mokondwa! Kuwa ndi chisangalalo, pakuti ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiri kuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena