Salimo 113:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuchititsa mkazi wosabereka kukhala m’nyumba+Monga mayi wosangalala wa ana aamuna.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Aroma 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+ Agalatiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+ Agalatiya 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Yerusalemu+ wam’mwamba ndi mfulu, ndipo ndiye mayi wathu.+ Chivumbulutso 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera m’fuko lililonse+ la ana a Isiraeli,+ anadindidwa chidindo:
9 Akuchititsa mkazi wosabereka kukhala m’nyumba+Monga mayi wosangalala wa ana aamuna.+Tamandani Ya, anthu inu!+
26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+
29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+
4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera m’fuko lililonse+ la ana a Isiraeli,+ anadindidwa chidindo: