Hoseya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anabwerera, koma sanapite ku chipembedzo choona.+ Anakhala ngati uta wosakungika.+ Akalonga awo adzaphedwa ndi lupanga chifukwa cha mwano wa lilime lawo lomwe.+ N’chifukwa chake iwo adzanyozedwa m’dziko la Iguputo.”+ Hoseya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+
16 Anabwerera, koma sanapite ku chipembedzo choona.+ Anakhala ngati uta wosakungika.+ Akalonga awo adzaphedwa ndi lupanga chifukwa cha mwano wa lilime lawo lomwe.+ N’chifukwa chake iwo adzanyozedwa m’dziko la Iguputo.”+
3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+