Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 122:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mafuko amapita kumeneko,+

      Mafuko a Ya,+

      Amapita kumeneko kukatamanda dzina la Yehova+

      Mogwirizana ndi lamulo loperekedwa kwa Isiraeli.+

  • Yesaya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu ochokera m’mitundu yosiyanasiyana adzabwera n’kunena kuti: “Bwerani+ anthu inu. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova. Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo. Iye akatiphunzitsa njira zake, ndipo ife tidzayenda m’njira zakezo.”+ Pakuti mu Ziyoni mudzatuluka malamulo ndipo mawu a Yehova adzatuluka mu Yerusalemu.+

  • Yesaya 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova wa makamu adzakonzera anthu a mitundu yonse+ m’phiri ili,+ phwando la zakudya zabwinozabwino,+ phwando la vinyo wokoma kwambiri,* phwando la zakudya zabwinozabwino zokhala ndi mafuta a m’mafupa,+ ndiponso la vinyo+ wokoma kwambiri, wosefedwa bwino.+

  • Yesaya 52:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu zako+ iwe Ziyoni. Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera.+ Pakuti mwa iwe simudzabweranso munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa.+

  • Yeremiya 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pa nthawiyo mzinda wa Yerusalemu adzautcha kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsira+ ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso mitima yawo yoipayo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena