Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+

      Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo.

  • Yesaya 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+

  • Yesaya 65:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Mmbulu+ ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi.+ Mkango udzadya udzu ngati ng’ombe yamphongo,+ ndipo njoka izidzadya fumbi.+ Zimenezi sizidzapweteka aliyense+ kapena kuwononga chilichonse m’phiri langa lonse loyera,”+ watero Yehova.

  • Danieli 2:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Pamenepo chitsulo, dongo, mkuwa, siliva ndi golide, zonsezi zinaphwanyikaphwanyika ndipo zinakhala ngati mankhusu* apamalo opunthirapo mbewu+ m’chilimwe. Mphepo inaziuluza moti sizinaonekenso.+ Koma mwala umene unamenya chifanizirocho unakhala phiri lalikulu ndipo linadzaza dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena