40 “‘Nyumba yonse ya Isiraeli idzanditumikira m’phiri langa loyera,+ phiri lalitali la m’dziko la Isiraeli,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Kumeneko ndidzasangalala nawo ndipo ndidzafuna zopereka zanu ndi nsembe zanu za zinthu zoyambirira kucha pa zinthu zanu zonse zopatulika.+