Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 56:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndidzawabweretsa kuphiri langa loyera+ ndi kuwasangalatsa m’nyumba yanga yopemphereramo.+ Nsembe zawo zopsereza zathunthu+ ndi nsembe zawo zina+ ndidzazilandira paguwa langa lansembe.+ Pakuti nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo anthu a mitundu yonse.”+

  • Mika 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu ochokera m’mitundu yosiyanasiyana adzabwera n’kunena kuti: “Bwerani+ anthu inu. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova. Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo.+ Iye akatiphunzitsa njira zake,+ ndipo ife tidzayenda m’njira zakezo.”+ Pakuti mu Ziyoni mudzatuluka malamulo ndipo mawu a Yehova adzatuluka mu Yerusalemu.+

  • Zekariya 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena