Ekisodo 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Monga momwe Yehova analamulira Mose, Aroni anaikadi mtsukowo patsogolo pa Umboni*+ kuti manawo asungidwe. Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
34 Monga momwe Yehova analamulira Mose, Aroni anaikadi mtsukowo patsogolo pa Umboni*+ kuti manawo asungidwe.
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+