Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+

  • Machitidwe 28:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo iwo anapangana naye tsiku, ndipo anabwera mwaunyinji kumene iye anali kukhala. Chotero kuyambira m’mawa mpaka madzulo, anawafotokozera nkhani yonse pochitira umboni mokwanira za ufumu wa Mulungu.+ Anachitira umboniwo mwa kugwiritsa ntchito mfundo zokopa zokhudza Yesu, kuchokera m’chilamulo cha Mose+ ndi mu Zolemba za aneneri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena