Deuteronomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+ Yeremiya 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+
13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+
21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+