Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova Mulungu wathu anachita nafe pangano ku Horebe.+ Deuteronomo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditakwera m’phiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita nanu,+ ndinakhala m’phirimo masiku 40, usana ndi usiku,+ (sindinadye mkate kapena kumwa madzi,) Aheberi 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Mulungu wakulamulani kuti mulisunge.”+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
9 Nditakwera m’phiri kukalandira miyala iwiri yosema,+ miyala ya pangano limene Yehova anachita nanu,+ ndinakhala m’phirimo masiku 40, usana ndi usiku,+ (sindinadye mkate kapena kumwa madzi,)