Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+ Agalatiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zinthu zimenezi zili ndi tanthauzo lophiphiritsira,+ pakuti azimayi amenewa akuimira mapangano awiri.+ Loyamba ndi pangano la paphiri la Sinai,+ limene limabereka ana oti akhale akapolo. Pangano limenelo ndiye Hagara uja.
7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+
24 Zinthu zimenezi zili ndi tanthauzo lophiphiritsira,+ pakuti azimayi amenewa akuimira mapangano awiri.+ Loyamba ndi pangano la paphiri la Sinai,+ limene limabereka ana oti akhale akapolo. Pangano limenelo ndiye Hagara uja.