Ekisodo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Kwera m’phiri muno ufike kwa ine ndi kukhala momwe muno, pakuti ndikufuna kukupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+ Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+ Ekisodo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+ Ekisodo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Sema miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija,+ ndipo ine ndidzalemba pamiyala yosemayo mawu amene anali pamiyala yoyamba ija,+ imene iwe unaswa.+
12 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Kwera m’phiri muno ufike kwa ine ndi kukhala momwe muno, pakuti ndikufuna kukupatsa miyala yosema imene ndalembapo chilamulo kuti ndiphunzitse anthu.”+
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+
19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+
34 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Sema miyala iwiri yofanana ndi yoyamba ija,+ ndipo ine ndidzalemba pamiyala yosemayo mawu amene anali pamiyala yoyamba ija,+ imene iwe unaswa.+