Salimo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+