Ezekieli 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Pakuti amuna inu mwalankhula zabodza ndipo mwaona masomphenya onama, ine ndithana nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Pakuti amuna inu mwalankhula zabodza ndipo mwaona masomphenya onama, ine ndithana nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”