Ezekieli 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga.+ Ndidzasolola lupanga langa m’chimake+ ndi kupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.+ Ezekieli 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aneneri a mumzindawo apaka laimu machimo a atsogoleriwo.+ Aona masomphenya onama+ ndipo akuloserera atsogoleriwo zinthu zabodza.+ Iwo akunena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.
3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga.+ Ndidzasolola lupanga langa m’chimake+ ndi kupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.+
28 Aneneri a mumzindawo apaka laimu machimo a atsogoleriwo.+ Aona masomphenya onama+ ndipo akuloserera atsogoleriwo zinthu zabodza.+ Iwo akunena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.