Ezekieli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Choncho uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Bwererani, siyani mafano anu onyansa.+ Tembenuzani nkhope zanu kuti musayang’anenso zinthu zanu zonse zonyansa.+
6 “Choncho uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Bwererani, siyani mafano anu onyansa.+ Tembenuzani nkhope zanu kuti musayang’anenso zinthu zanu zonse zonyansa.+