Ezekieli 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 chifukwa anakana zigamulo zanga, sanayende motsatira malamulo anga, anadetsa sabata langa komanso mtima wawo unali pa mafano awo onyansa.+
16 chifukwa anakana zigamulo zanga, sanayende motsatira malamulo anga, anadetsa sabata langa komanso mtima wawo unali pa mafano awo onyansa.+