Ezekieli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+
8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+