Ezekieli 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘“Zombo za ku Tarisi+ zoyenda m’gulu limodzi zinali kunyamula katundu wako wamalonda. Choncho unalemera ndi kukhala waulemerero kwambiri pakati pa nyanja.+
25 “‘“Zombo za ku Tarisi+ zoyenda m’gulu limodzi zinali kunyamula katundu wako wamalonda. Choncho unalemera ndi kukhala waulemerero kwambiri pakati pa nyanja.+