Ezekieli 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano nyanja yakuwononga, ndipo wamira m’madzi ozama.+ Katundu wako wamalonda ndi khamu la anthu+ limene linali mwa iwe zatheratu.
34 Tsopano nyanja yakuwononga, ndipo wamira m’madzi ozama.+ Katundu wako wamalonda ndi khamu la anthu+ limene linali mwa iwe zatheratu.