Ezekieli 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dziko la Iguputo lidzakhala bwinja ndi malo owonongeka.+ Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova chifukwa chakuti iwe Farao wanena kuti, ‘Mtsinje wa Nailo ndi wanga, ndipo ineyo ndinaupanga ndekha.’+
9 Dziko la Iguputo lidzakhala bwinja ndi malo owonongeka.+ Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova chifukwa chakuti iwe Farao wanena kuti, ‘Mtsinje wa Nailo ndi wanga, ndipo ineyo ndinaupanga ndekha.’+