Ezekieli 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dziko la Iguputo lidzakhala malo owonongeka komanso bwinja.+ Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, chifukwa chakuti iwe wanena kuti,* ‘Mtsinje wa Nailo ndi wanga. Ineyo ndinaupanga ndekha.’+
9 Dziko la Iguputo lidzakhala malo owonongeka komanso bwinja.+ Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, chifukwa chakuti iwe wanena kuti,* ‘Mtsinje wa Nailo ndi wanga. Ineyo ndinaupanga ndekha.’+