Ezekieli 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho ndinawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu, moti anamwazikira m’mayiko osiyanasiyana.+ Ndinawaweruza mogwirizana ndi njira zawo komanso zochita zawo.+
19 Choncho ndinawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu, moti anamwazikira m’mayiko osiyanasiyana.+ Ndinawaweruza mogwirizana ndi njira zawo komanso zochita zawo.+