Ezekieli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano mapeto akufikira,+ ndipo ndikutumizira mkwiyo wanga. Ndikuweruza mogwirizana ndi njira zako+ ndipo ndikubwezera chifukwa cha zonyansa zako zonse. Ezekieli 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Chotero ine ndidzaweruza aliyense wa inu malinga ndi njira zake,+ inu a nyumba ya Isiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Lapani ndi kusiya zolakwa zanu zonse+ ndipo musalole kuti chilichonse chizikupunthwitsani ndi kukulakwitsani.+ Ezekieli 39:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndinawachitira zinthu mogwirizana ndi zonyansa zimene anachita komanso chifukwa chakuti anaphwanya malamulo,+ moti ndinawabisira nkhope yanga.’
3 Tsopano mapeto akufikira,+ ndipo ndikutumizira mkwiyo wanga. Ndikuweruza mogwirizana ndi njira zako+ ndipo ndikubwezera chifukwa cha zonyansa zako zonse.
30 “‘Chotero ine ndidzaweruza aliyense wa inu malinga ndi njira zake,+ inu a nyumba ya Isiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Lapani ndi kusiya zolakwa zanu zonse+ ndipo musalole kuti chilichonse chizikupunthwitsani ndi kukulakwitsani.+
24 Ndinawachitira zinthu mogwirizana ndi zonyansa zimene anachita komanso chifukwa chakuti anaphwanya malamulo,+ moti ndinawabisira nkhope yanga.’