7 Chipinda cha alonda chinali bango limodzi m’litali ndi bango limodzi m’lifupi. Kuchokera pachipinda cha alonda kukafika pachipinda china cha alonda+ panali mikono isanu. Malo apafupi ndi khomo la kanyumbako, pafupi ndi khonde lamkati anali bango limodzi.