-
Ezekieli 40:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Zipinda za alondazo komanso zipilala zimene zinali m’mbali mwa zipindazo zinali ndi mawindo okhala ndi mafelemu aakulu mkati koma aang’ono kunja+ kuzungulira kanyumba konseko. Umu ndi mmenenso zinalili ndi mawindo apakhonde. Mkati mwa kanyumbako munali mawindo aakulu mkati, kuzungulira mbali zonse ndipo pazipilala zam’mbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza.+
-