-
Ezekieli 40:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Chipata cha bwalo lamkati chinayang’anizana ndi chipata cha kumpoto. Chipata cha kum’mawa cha bwalo lamkati nachonso chinayang’anizana ndi chipata cha kum’mawa. Munthu uja anayezanso mikono 100 kuchokera pachipata kukafika pachipata china.
-