-
Ezekieli 40:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Khonde lake linayang’ana kubwalo lakunja. Pazipilala zake zam’mbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza kumbali iyi ndi kumbali inayo, ndipo masitepe olowera m’kanyumba ka pachipatako analipo 8.
-