-
Ezekieli 40:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Munthu uja anayezanso bwalo lamkati. Iye anapeza kuti m’litali mwake, linali mikono 100 ndipo m’lifupi linalinso mikono 100. Bwalolo linali lofanana mbali zonse zinayi. Kutsogolo kwa nyumbayo kunali guwa lansembe.
-