Danieli 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kumasulira kwa mawuwa ndi uku: MENE, Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo waumaliza.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:26 Ulosi wa Danieli, tsa. 108