Danieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:9 Ulosi wa Danieli, tsa. 289
9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+