Danieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, chifukwa mawuwa akuyenera kusungidwa mwachinsinsi ndi kumatidwa mpaka nthawi yamapeto.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:9 Ulosi wa Danieli, tsa. 289
9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, chifukwa mawuwa akuyenera kusungidwa mwachinsinsi ndi kumatidwa mpaka nthawi yamapeto.+