Hoseya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+
4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+