Hoseya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye ndi Yehova Mulungu wa makamu.+ Yehova ndilo dzina lake lomukumbukira nalo.+