Hoseya 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Koma ndidzakuchititsa kukhala m’mahema ngati pa masiku achikondwerero.
9 “Ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Koma ndidzakuchititsa kukhala m’mahema ngati pa masiku achikondwerero.