Yoweli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 15-16
12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+