Mika 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Tsiku la Yehova, ptsa. 115-116, 117-120
12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+