Nahumu 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova adzakweza ulemu wa Yakobo+ ndi kubwezeretsa ulemerero wa Isiraeli. Pakuti owononga awawononga,+ ndipo mphukira zawo zasakazidwa.+
2 Pamenepo Yehova adzakweza ulemu wa Yakobo+ ndi kubwezeretsa ulemerero wa Isiraeli. Pakuti owononga awawononga,+ ndipo mphukira zawo zasakazidwa.+