Salimo 47:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzatisankhira cholowa,+Chimene Yakobo, amene amamukonda, anakondwera nacho.+ [Seʹlah.] Amosi 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+
7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+