Nahumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera pamene Nineve anakhalapo,+ iye wakhala ngati dziwe la madzi,+ koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Imani amuna inu! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.+ Nahumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Galamukani!,12/2010, tsa. 28
8 Kuchokera pamene Nineve anakhalapo,+ iye wakhala ngati dziwe la madzi,+ koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Imani amuna inu! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.+