Habakuku 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Tsoka kwa munthu amene akuuza chidutswa cha mtengo kuti: “Dzuka!” Amene amauzanso mwala wosalankhula kuti: “Dzuka! Tipatse malangizo”!+ Taona! Fanolo ndi lokutidwa ndi golide ndi siliva+ ndipo mulibe mpweya* mkati mwake.+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, ptsa. 18-19
19 “‘Tsoka kwa munthu amene akuuza chidutswa cha mtengo kuti: “Dzuka!” Amene amauzanso mwala wosalankhula kuti: “Dzuka! Tipatse malangizo”!+ Taona! Fanolo ndi lokutidwa ndi golide ndi siliva+ ndipo mulibe mpweya* mkati mwake.+