Zefaniya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wachotsa zigamulo zake pa iwe.+ Watembenuza ndi kubweza mdani wako.+ Mfumu ya Isiraeli, Yehova, ali pakati pa anthu ako+ ndipo sudzaopanso kuti tsoka likugwera.+
15 Yehova wachotsa zigamulo zake pa iwe.+ Watembenuza ndi kubweza mdani wako.+ Mfumu ya Isiraeli, Yehova, ali pakati pa anthu ako+ ndipo sudzaopanso kuti tsoka likugwera.+