Zekariya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+
5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+