Salimo 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndidzawapera kukhala ngati fumbi louluzika ndi mphepo.+Ndidzawakhuthula ngati matope a mumsewu.+ Mika 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani wanga adzaona zimenezi, ndipo amene anali kunena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ adzachita manyazi.+ Maso anga adzamuyang’ana.+ Iye adzakhala malo opondedwapondedwa ngati matope a mumsewu.+
10 Mdani wanga adzaona zimenezi, ndipo amene anali kunena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ adzachita manyazi.+ Maso anga adzamuyang’ana.+ Iye adzakhala malo opondedwapondedwa ngati matope a mumsewu.+