Yesaya 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+ ndipo ndidzamulamula kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa. Ndidzamuuza+ kuti akalande zinthu zambiri, akatenge katundu wambiri, ndiponso akapondeponde anthuwo ngati matope a mumsewu.+ Zekariya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+ Malaki 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu inu mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kumapazi anu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,”+ watero Yehova wa makamu.
6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+ ndipo ndidzamulamula kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa. Ndidzamuuza+ kuti akalande zinthu zambiri, akatenge katundu wambiri, ndiponso akapondeponde anthuwo ngati matope a mumsewu.+
5 Onsewa adzakhala ngati amuna amphamvu+ opondaponda matope a m’misewu ya kunkhondo.+ Iwo adzamenya nkhondo pakuti Yehova ali nawo.+ Adani awo oyenda pamahatchi adzachita manyazi.+
3 “Anthu inu mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kumapazi anu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,”+ watero Yehova wa makamu.