Zekariya 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Ndidzawaitana ndi likhweru+ ndi kuwasonkhanitsa pamodzi. Ndithu ine ndidzawawombola,+ ndipo iwo adzachuluka ngati anthu amene kale anali ambiri.+
8 “‘Ndidzawaitana ndi likhweru+ ndi kuwasonkhanitsa pamodzi. Ndithu ine ndidzawawombola,+ ndipo iwo adzachuluka ngati anthu amene kale anali ambiri.+