Mateyu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Yesu atamva kuti Yohane amugwira,+ anachoka kumeneko ndipo anapita ku Galileya.+