Mateyu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yake angaibwezeretse motani? Sungagwire ntchito iliyonse koma ungafunike kuutaya kunja+ kumene anthu akaupondaponda. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 86, 197 Nsanja ya Olonda,12/1/2012, tsa. 215/1/2012, ptsa. 4, 8-95/1/2009, tsa. 1412/15/1999, tsa. 308/15/1999, tsa. 321/1/1989, tsa. 93/15/1987, tsa. 11
13 “Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yake angaibwezeretse motani? Sungagwire ntchito iliyonse koma ungafunike kuutaya kunja+ kumene anthu akaupondaponda.
5:13 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 86, 197 Nsanja ya Olonda,12/1/2012, tsa. 215/1/2012, ptsa. 4, 8-95/1/2009, tsa. 1412/15/1999, tsa. 308/15/1999, tsa. 321/1/1989, tsa. 93/15/1987, tsa. 11